Salimo 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Aliyense wopanda mlandu m’manja mwake ndi woyera mumtima mwake,+Amene sanaone Moyo wanga ngati wopanda pake,+Kapena kulumbira mwachinyengo.+ Salimo 73:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 73 Mulungu ndi wabwinodi kwa Isiraeli, kwa anthu oyera mtima.+ Miyambo 22:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Amene amakondwera kukhala ndi mtima woyera+ ndiponso amene mawu ake ndi okopa, adzakhala bwenzi la mfumu.+ Tito 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zinthu zonse n’zoyera kwa anthu oyera.+ Koma kwa anthu oipitsidwa+ ndi opanda chikhulupiriro+ kulibe choyera, m’malomwake maganizo awo ndi chikumbumtima+ chawo n’zoipa.
4 Aliyense wopanda mlandu m’manja mwake ndi woyera mumtima mwake,+Amene sanaone Moyo wanga ngati wopanda pake,+Kapena kulumbira mwachinyengo.+
11 Amene amakondwera kukhala ndi mtima woyera+ ndiponso amene mawu ake ndi okopa, adzakhala bwenzi la mfumu.+
15 Zinthu zonse n’zoyera kwa anthu oyera.+ Koma kwa anthu oipitsidwa+ ndi opanda chikhulupiriro+ kulibe choyera, m’malomwake maganizo awo ndi chikumbumtima+ chawo n’zoipa.