Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 22:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Yehova amandipatsa mphoto mogwirizana ndi chilungamo changa.+

      Amandibwezera mogwirizana ndi kuyera kwa manja anga.+

  • Salimo 37:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Khulupirira Yehova ndipo chita zabwino.+

      Khala padziko lapansi, ndipo khala wokhulupirika m’zochita zako zonse.+

  • Yesaya 33:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Pali munthu amene amayenda m’chilungamo nthawi zonse,+ amene amalankhula zowongoka,+ amene amakana kupeza phindu mwachinyengo,+ amene salola kuti manja ake alandire chiphuphu,+ amene amatseka makutu ake kuti asamve nkhani zokhudza kukhetsa magazi, ndiponso amene amatseka maso ake kuti asaone zoipa.+

  • Mateyu 5:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Odala ndi anthu oyera mtima,+ chifukwa adzaona Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena