Salimo 106:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Odala ndi anthu amene amatsata chilungamo,+Ndi kuchita zolungama nthawi zonse.+ Ezekieli 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iye sapondereza munthu wosautsika. Sakongoza zinthu mwa katapira+ ndipo salandira chiwongoladzanja.+ Amatsatira zigamulo zanga+ ndi kuyenda motsatira malamulo anga.+ Munthu wotere sadzafa chifukwa cha zolakwa za bambo ake.+ Adzakhalabe ndi moyo.+ Malaki 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Lamulo la choonadi linali m’kamwa mwake+ ndipo pamilomo pake panalibe zosalungama. Anali kuyenda ndi ine mwamtendere komanso mowongoka mtima,+ ndipo anabweza anthu ambiri panjira zawo zolakwika.+
17 Iye sapondereza munthu wosautsika. Sakongoza zinthu mwa katapira+ ndipo salandira chiwongoladzanja.+ Amatsatira zigamulo zanga+ ndi kuyenda motsatira malamulo anga.+ Munthu wotere sadzafa chifukwa cha zolakwa za bambo ake.+ Adzakhalabe ndi moyo.+
6 Lamulo la choonadi linali m’kamwa mwake+ ndipo pamilomo pake panalibe zosalungama. Anali kuyenda ndi ine mwamtendere komanso mowongoka mtima,+ ndipo anabweza anthu ambiri panjira zawo zolakwika.+