Ekisodo 32:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno Mose anakaima pachipata cha msasawo, ndipo anati: “Ndani ali kumbali ya Yehova? Abwere kwa ine!”+ Ndipo ana onse aamuna a Levi anayamba kusonkhana kwa Mose.
26 Ndiyeno Mose anakaima pachipata cha msasawo, ndipo anati: “Ndani ali kumbali ya Yehova? Abwere kwa ine!”+ Ndipo ana onse aamuna a Levi anayamba kusonkhana kwa Mose.