Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 24:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ngati kutumikira Yehova kukukuipirani, sankhani lero amene mukufuna kum’tumikira,+ kaya milungu imene makolo anu amene anali kutsidya lina la Mtsinje anatumikira,+ kapena milungu ya Aamori amene mukukhala m’dziko lawo.+ Koma ine ndi a m’nyumba yanga, tizitumikira Yehova.”+

  • 2 Mafumu 9:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Yehu atamva mawu amenewa, anakweza maso kuyang’ana pawindopo, n’kufunsa kuti: “Ndani ali kumbali yanga? Ndani?”+ Nthawi yomweyo nduna ziwiri kapena zitatu za panyumba ya mfumu+ zinasuzumira pansi kuyang’ana Yehu.

  • 2 Mafumu 10:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yehu atachoka pamenepo, anakumana ndi Yehonadabu+ mwana wa Rekabu+ akubwera kudzakumana naye. Atamudalitsa,+ anam’funsa kuti: “Kodi mtima wako ndi wogwirizana ndi ine mopanda chinyengo, monga momwe mtima wanga ulili ndi mtima wako?”+

      Yehonadabu anayankha kuti: “Inde, ndi wotero.”

      Ndiyeno Yehu anati: “Ngati ndi wotero, ndipatse dzanja lako.”

      Choncho Yehonadabu anapereka dzanja lake, ndipo Yehu anamukweza m’galeta lake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena