Genesis 47:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako Yosefe anabweretsa bambo ake Yakobo n’kuwasonyeza kwa Farao. Ndipo Yakobo anadalitsa Farao.+ Numeri 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Lankhula ndi Aroni ndiponso ana ake kuti, ‘Muzidalitsa+ ana a Isiraeli motere: Rute 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako Boazi anafika kuchokera ku Betelehemu ndipo anauza okololawo kuti: “Yehova akhale nanu.”+ Iwo anayankha mwa nthawi zonse kuti: “Yehova akudalitseni.”+ Aroma 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pitirizani kudalitsa anthu amene amakuzunzani.+ Muzidalitsa,+ osatemberera ayi.+
7 Kenako Yosefe anabweretsa bambo ake Yakobo n’kuwasonyeza kwa Farao. Ndipo Yakobo anadalitsa Farao.+
4 Kenako Boazi anafika kuchokera ku Betelehemu ndipo anauza okololawo kuti: “Yehova akhale nanu.”+ Iwo anayankha mwa nthawi zonse kuti: “Yehova akudalitseni.”+