Oweruza 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo mngelo wa Yehova anaonekera kwa iye, ndipo anati: “Yehova ali ndi iwe,+ munthu wolimba mtima ndi wamphamvuwe.” 2 Timoteyo 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ambuye akhale nawe chifukwa cha mzimu umene umaonetsa.+ Kukoma mtima kwake kwakukulu kukhale nanu.
12 Pamenepo mngelo wa Yehova anaonekera kwa iye, ndipo anati: “Yehova ali ndi iwe,+ munthu wolimba mtima ndi wamphamvuwe.”
22 Ambuye akhale nawe chifukwa cha mzimu umene umaonetsa.+ Kukoma mtima kwake kwakukulu kukhale nanu.