Agalatiya 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Abale, kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye wathu Yesu Khristu, kukhale nanu chifukwa cha mzimu+ umene mumausonyeza. Ame. Filimoni 25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye Yesu Khristu kukhale nanu chifukwa cha mzimu umene mumaonetsa.+
18 Abale, kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye wathu Yesu Khristu, kukhale nanu chifukwa cha mzimu+ umene mumausonyeza. Ame.