2 Timoteyo 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ambuye akhale nawe chifukwa cha mzimu umene umaonetsa.+ Kukoma mtima kwake kwakukulu kukhale nanu. Filimoni 25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye Yesu Khristu kukhale nanu chifukwa cha mzimu umene mumaonetsa.+
22 Ambuye akhale nawe chifukwa cha mzimu umene umaonetsa.+ Kukoma mtima kwake kwakukulu kukhale nanu.