Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 32:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ndiyeno Mose anakaima pachipata cha msasawo, ndipo anati: “Ndani ali kumbali ya Yehova? Abwere kwa ine!”+ Ndipo ana onse aamuna a Levi anayamba kusonkhana kwa Mose.

  • 1 Mbiri 12:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Poyankha, Amasai mkulu wa asilikali 30 anagwidwa ndi mzimu,+ ndipo anati:

      “Ifetu ndife anthu anu, inu a Davide, ndipotu tili kumbali yanu,+ inu mwana wa Jese.

      Mtendere ukhale nanu, ndiponso mtendere ukhale ndi iye amene akukuthandizani,

      Pakuti Mulungu wanu wakuthandizani.”+

      Choncho Davide anawalandira ndi kuwaika pakati pa atsogoleri a asilikali.+

  • Salimo 94:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndani adzanyamuka kuti amenye nkhondo ndi anthu ochita zoipa m’malo mwa ine?+

      Ndani adzaima m’malo mwa ine kulimbana ndi anthu ochita zopweteka anzawo?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena