2 Samueli 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma Itai anayankha mfumu kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo, komanso pali moyo wanu mbuyanga mfumu,+ kulikonse kumene inu mbuyanga mfumu mudzapita ine mtumiki wanu ndidzapitanso komweko, ndipo ndili wokonzeka ngakhale kufa nanu limodzi!”+
21 Koma Itai anayankha mfumu kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo, komanso pali moyo wanu mbuyanga mfumu,+ kulikonse kumene inu mbuyanga mfumu mudzapita ine mtumiki wanu ndidzapitanso komweko, ndipo ndili wokonzeka ngakhale kufa nanu limodzi!”+