Salimo 54:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Taonani! Mulungu ndiye mthandizi wanga.+Yehova ali pakati pa anthu amene akuchirikiza moyo wanga.