-
1 Mbiri 12:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Poyankha, Amasai mkulu wa asilikali 30 anagwidwa ndi mzimu,+ ndipo anati:
“Ifetu ndife anthu anu, inu a Davide, ndipotu tili kumbali yanu,+ inu mwana wa Jese.
Mtendere ukhale nanu, ndiponso mtendere ukhale ndi iye amene akukuthandizani,
Pakuti Mulungu wanu wakuthandizani.”+
Choncho Davide anawalandira ndi kuwaika pakati pa atsogoleri a asilikali.+
-