Aheberi 10:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Tsopano, ife si mtundu wa anthu obwerera m’mbuyo kupita kuchiwonongeko,+ koma mtundu wa anthu okhala ndi chikhulupiriro chosunga moyo.+ Yakobo 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma azipempha+ ndi chikhulupiriro, osakayikira m’pang’ono pomwe,+ pakuti wokayikira ali ngati funde lapanyanja lotengeka ndi mphepo+ ndi lowindukawinduka.
39 Tsopano, ife si mtundu wa anthu obwerera m’mbuyo kupita kuchiwonongeko,+ koma mtundu wa anthu okhala ndi chikhulupiriro chosunga moyo.+
6 Koma azipempha+ ndi chikhulupiriro, osakayikira m’pang’ono pomwe,+ pakuti wokayikira ali ngati funde lapanyanja lotengeka ndi mphepo+ ndi lowindukawinduka.