2 Petulo 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndithudi, ngati anapulumuka ku zoipitsa za dzikoli+ mwa kumudziwa molondola Ambuye ndi Mpulumutsi Yesu Khristu, koma alowereranso m’zinthu zomwe zija ndi kugonjetsedwa nazo,+ potsirizira pake makhalidwe awo amakhala oipa kwambiri kuposa poyamba.+
20 Ndithudi, ngati anapulumuka ku zoipitsa za dzikoli+ mwa kumudziwa molondola Ambuye ndi Mpulumutsi Yesu Khristu, koma alowereranso m’zinthu zomwe zija ndi kugonjetsedwa nazo,+ potsirizira pake makhalidwe awo amakhala oipa kwambiri kuposa poyamba.+