Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 12:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Ukatero umapita kukatenga mizimu ina 7 yoipa kwambiri kuposa umenewo.+ Ikalowa mkatimo imakhala mmenemo ndipo potsirizira pake zochita za munthuyo zimakhala zoipa kwambiri kuposa poyamba.+ Ndi mmenenso zidzakhalira ndi m’badwo woipawu.”+

  • Luka 11:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Kenako umapita kukatenga mizimu ina 7+ yoipa kwambiri kuposa umenewu, ndipo ikalowa mkatimo, imakhala mmenemo. Potsirizira pake zochita za munthu ameneyu zimakhala zoipa kwambiri kuposa poyamba paja.”+

  • Aheberi 10:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Pakuti ngati tikuchita machimo mwadala+ pambuyo podziwa choonadi molondola,+ palibe nsembe ina yotsala imene ingaperekedwe chifukwa cha machimo athuwo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena