Aheberi 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pali anthu amene Mulungu anawaunikira,+ amene analawa mphatso yaulere yakumwamba,+ amene analandira mzimu woyera,+ 2 Petulo 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Zikanakhala bwino akanapanda kudziwa molondola njira ya chilungamo,+ kusiyana n’kuidziwa bwinobwino kenako n’kupatuka pa lamulo loyera lomwe anapatsidwa.+
4 Pali anthu amene Mulungu anawaunikira,+ amene analawa mphatso yaulere yakumwamba,+ amene analandira mzimu woyera,+
21 Zikanakhala bwino akanapanda kudziwa molondola njira ya chilungamo,+ kusiyana n’kuidziwa bwinobwino kenako n’kupatuka pa lamulo loyera lomwe anapatsidwa.+