Mateyu 12:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mwachitsanzo, aliyense wolankhula mawu onyoza Mwana wa munthu, adzakhululukidwa.+ Koma aliyense wolankhula monyoza mzimu woyera, sadzakhululukidwa, m’nthawi* ino kapena ikubwerayo.+ Yohane 9:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Yesu anati: “Mukanakhala akhungu, simukanakhala ndi tchimo. Koma popeza mukunena kuti, ‘Tikuona.’+ Tchimo+ lanu likhalabe chikhalire.” Aheberi 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 koma tsopano anagwa.+ Anthu amenewa n’zosatheka kuwadzutsanso kuti alape.+ N’zosatheka chifukwa chakuti anthu amenewa akupachika kachiwiri Mwana wa Mulungu ndi kumunyoza poyera.+
32 Mwachitsanzo, aliyense wolankhula mawu onyoza Mwana wa munthu, adzakhululukidwa.+ Koma aliyense wolankhula monyoza mzimu woyera, sadzakhululukidwa, m’nthawi* ino kapena ikubwerayo.+
41 Yesu anati: “Mukanakhala akhungu, simukanakhala ndi tchimo. Koma popeza mukunena kuti, ‘Tikuona.’+ Tchimo+ lanu likhalabe chikhalire.”
6 koma tsopano anagwa.+ Anthu amenewa n’zosatheka kuwadzutsanso kuti alape.+ N’zosatheka chifukwa chakuti anthu amenewa akupachika kachiwiri Mwana wa Mulungu ndi kumunyoza poyera.+