Miyambo 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kodi waona munthu wodziona ngati wanzeru m’maso mwake?+ Munthu wopusa ali ndi chiyembekezo chachikulu+ kuposa iyeyo. 2 Akorinto 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakati pa anthu amenewa, mulungu wa nthawi* ino+ wachititsa khungu maganizo a anthu osakhulupirira,+ kuti asaone+ kuwala+ kwa uthenga wabwino waulemerero+ wonena za Khristu, yemwe ali chifaniziro+ cha Mulungu.
12 Kodi waona munthu wodziona ngati wanzeru m’maso mwake?+ Munthu wopusa ali ndi chiyembekezo chachikulu+ kuposa iyeyo.
4 Pakati pa anthu amenewa, mulungu wa nthawi* ino+ wachititsa khungu maganizo a anthu osakhulupirira,+ kuti asaone+ kuwala+ kwa uthenga wabwino waulemerero+ wonena za Khristu, yemwe ali chifaniziro+ cha Mulungu.