Miyambo 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Njira ya munthu wopusa imakhala yolondola m’maso mwake,+ koma womvera malangizo ndi wanzeru.+ Aroma 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Muziona ena mmene inuyo mumadzionera.+ Musamaganize modzikweza,+ koma khalani ndi mtima wodzichepetsa.+ Musadziyese anzeru.+ 1 Akorinto 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu asamadzinyenge yekha: Ngati aliyense wa inu akudziyesa wanzeru+ mu nthawi* ino, akhale wopusa kuti akhale wanzeru.+ 1 Akorinto 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ngati wina akuganiza kuti akudziwa za chinachake,+ sanachidziwebe mokwanira.+
16 Muziona ena mmene inuyo mumadzionera.+ Musamaganize modzikweza,+ koma khalani ndi mtima wodzichepetsa.+ Musadziyese anzeru.+
18 Munthu asamadzinyenge yekha: Ngati aliyense wa inu akudziyesa wanzeru+ mu nthawi* ino, akhale wopusa kuti akhale wanzeru.+