Danieli 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Anthu ozindikira adzawala ngati kuwala kwa kuthambo.+ Ndipo amene akuthandiza anthu ambiri kukhala olungama+ adzawala ngati nyenyezi mpaka kalekale, inde, kwamuyaya. Danieli 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu ambiri adzadzitsuka,+ adzadziyeretsa+ ndipo adzayengedwa.+ Anthu oipa adzachita zinthu zoipa+ ndipo palibe munthu woipa aliyense amene adzamvetsetse mawu amenewa,+ koma anthu ozindikira adzawamvetsetsa.+
3 “Anthu ozindikira adzawala ngati kuwala kwa kuthambo.+ Ndipo amene akuthandiza anthu ambiri kukhala olungama+ adzawala ngati nyenyezi mpaka kalekale, inde, kwamuyaya.
10 Anthu ambiri adzadzitsuka,+ adzadziyeretsa+ ndipo adzayengedwa.+ Anthu oipa adzachita zinthu zoipa+ ndipo palibe munthu woipa aliyense amene adzamvetsetse mawu amenewa,+ koma anthu ozindikira adzawamvetsetsa.+