Miyambo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Usamadzione kuti ndiwe wanzeru.+ Uziopa Yehova ndi kupatuka pa choipa.+ Luka 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Bwana wake uja anamuyamikira mtumiki ameneyu, ngakhale kuti anali wosalungama, chifukwa anachita mwanzeru.+ Pakuti ana a m’dziko lino amachita mwanzeru pochita zinthu ndi anthu a m’badwo wawo kuposa ana a kuwala.+
8 Bwana wake uja anamuyamikira mtumiki ameneyu, ngakhale kuti anali wosalungama, chifukwa anachita mwanzeru.+ Pakuti ana a m’dziko lino amachita mwanzeru pochita zinthu ndi anthu a m’badwo wawo kuposa ana a kuwala.+