Aheberi 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma tsopano anthu amenewa anagwa+ ndipo nʼzosatheka kuwadzutsanso kuti alape, chifukwa akupachika kachiwiri Mwana wa Mulungu ndiponso kumunyoza poyera.+
6 Koma tsopano anthu amenewa anagwa+ ndipo nʼzosatheka kuwadzutsanso kuti alape, chifukwa akupachika kachiwiri Mwana wa Mulungu ndiponso kumunyoza poyera.+