1 Yohane 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Amenewo anachoka pakati pathu, koma sanali mʼgulu lathu,*+ chifukwa akanakhala a mʼgulu lathu, akanakhalabe ndi ife. Koma anachoka kuti zidziwike kuti si onse amene ali mʼgulu lathu.+
19 Amenewo anachoka pakati pathu, koma sanali mʼgulu lathu,*+ chifukwa akanakhala a mʼgulu lathu, akanakhalabe ndi ife. Koma anachoka kuti zidziwike kuti si onse amene ali mʼgulu lathu.+