1 Yohane 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Amenewo anachoka pakati pathu, koma sanali m’gulu lathu,+ chifukwa akanakhala a m’gulu lathu, akanakhalabe ndi ife.+ Sikuti onse ali m’gulu lathu ayi, ndipo iwo achoka m’gulu lathu, kuti zimenezi zidziwike.+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:19 Nsanja ya Olonda,6/1/2015, tsa. 141/15/1987, tsa. 30
19 Amenewo anachoka pakati pathu, koma sanali m’gulu lathu,+ chifukwa akanakhala a m’gulu lathu, akanakhalabe ndi ife.+ Sikuti onse ali m’gulu lathu ayi, ndipo iwo achoka m’gulu lathu, kuti zimenezi zidziwike.+