1 Yohane 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Amenewo anachoka pakati pathu, koma sanali mʼgulu lathu,*+ chifukwa akanakhala a mʼgulu lathu, akanakhalabe ndi ife. Koma anachoka kuti zidziwike kuti si onse amene ali mʼgulu lathu.+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:19 Nsanja ya Olonda,6/1/2015, tsa. 141/15/1987, tsa. 30
19 Amenewo anachoka pakati pathu, koma sanali mʼgulu lathu,*+ chifukwa akanakhala a mʼgulu lathu, akanakhalabe ndi ife. Koma anachoka kuti zidziwike kuti si onse amene ali mʼgulu lathu.+