Maliko 3:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Komabe, aliyense amene wanyoza mzimu woyera sadzakhululukidwa kwamuyaya, koma adzakhala ndi mlandu wa tchimo losatha.”+ Luka 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo aliyense wonena mawu onyoza Mwana wa munthu, adzakhululukidwa. Koma wonyoza mzimu woyera sadzakhululukidwa.+ Aheberi 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pakuti ngati tikuchita machimo mwadala+ pambuyo podziwa choonadi molondola,+ palibe nsembe ina yotsala imene ingaperekedwe chifukwa cha machimo athuwo.+
29 Komabe, aliyense amene wanyoza mzimu woyera sadzakhululukidwa kwamuyaya, koma adzakhala ndi mlandu wa tchimo losatha.”+
10 Ndipo aliyense wonena mawu onyoza Mwana wa munthu, adzakhululukidwa. Koma wonyoza mzimu woyera sadzakhululukidwa.+
26 Pakuti ngati tikuchita machimo mwadala+ pambuyo podziwa choonadi molondola,+ palibe nsembe ina yotsala imene ingaperekedwe chifukwa cha machimo athuwo.+