Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 12:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Mwachitsanzo, aliyense wolankhula mawu onyoza Mwana wa munthu, adzakhululukidwa.+ Koma aliyense wolankhula monyoza mzimu woyera, sadzakhululukidwa, m’nthawi* ino kapena ikubwerayo.+

  • Aheberi 6:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pali anthu amene Mulungu anawaunikira,+ amene analawa mphatso yaulere yakumwamba,+ amene analandira mzimu woyera,+

  • Aheberi 6:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 koma tsopano anagwa.+ Anthu amenewa n’zosatheka kuwadzutsanso kuti alape.+ N’zosatheka chifukwa chakuti anthu amenewa akupachika kachiwiri Mwana wa Mulungu ndi kumunyoza poyera.+

  • Aheberi 10:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Pakuti ngati tikuchita machimo mwadala+ pambuyo podziwa choonadi molondola,+ palibe nsembe ina yotsala imene ingaperekedwe chifukwa cha machimo athuwo.+

  • 1 Yohane 5:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ngati wina waona m’bale wake akuchita tchimo losabweretsa imfa,+ amupempherere, ndipo Mulungu adzamupatsa moyo.+ Panotu ndikunena za ochita machimo osabweretsa imfa.+ Koma palinso tchimo lobweretsa imfa. Ndipo sindikunena kuti mupempherere munthu amene wachita tchimo loterolo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena