Mateyu 12:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mwachitsanzo, aliyense wolankhula mawu onyoza Mwana wa munthu, adzakhululukidwa.+ Koma aliyense wolankhula monyoza mzimu woyera, sadzakhululukidwa, m’nthawi* ino kapena ikubwerayo.+
32 Mwachitsanzo, aliyense wolankhula mawu onyoza Mwana wa munthu, adzakhululukidwa.+ Koma aliyense wolankhula monyoza mzimu woyera, sadzakhululukidwa, m’nthawi* ino kapena ikubwerayo.+