Salimo 119:118 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 118 Onse osochera ndi kuchoka pa malangizo anu mwawataya kutali,+Pakuti ndi achinyengo komanso onama.+ 2 Akorinto 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti amuna oterowo ndi atumwi onama, antchito achinyengo,+ odzisandutsa atumwi a Khristu.+ Aheberi 10:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Tsopano, ife si mtundu wa anthu obwerera m’mbuyo kupita kuchiwonongeko,+ koma mtundu wa anthu okhala ndi chikhulupiriro chosunga moyo.+ 1 Yohane 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Amenewo anachoka pakati pathu, koma sanali m’gulu lathu,+ chifukwa akanakhala a m’gulu lathu, akanakhalabe ndi ife.+ Sikuti onse ali m’gulu lathu ayi, ndipo iwo achoka m’gulu lathu, kuti zimenezi zidziwike.+
118 Onse osochera ndi kuchoka pa malangizo anu mwawataya kutali,+Pakuti ndi achinyengo komanso onama.+
39 Tsopano, ife si mtundu wa anthu obwerera m’mbuyo kupita kuchiwonongeko,+ koma mtundu wa anthu okhala ndi chikhulupiriro chosunga moyo.+
19 Amenewo anachoka pakati pathu, koma sanali m’gulu lathu,+ chifukwa akanakhala a m’gulu lathu, akanakhalabe ndi ife.+ Sikuti onse ali m’gulu lathu ayi, ndipo iwo achoka m’gulu lathu, kuti zimenezi zidziwike.+