Aroma 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti anthu oterowo si akapolo a Ambuye wathu Khristu, koma a mimba zawo.+ Ndipo mwa kulankhula mawu okopa+ ndi achinyengo+ amanyenga anthu oona mtima. 2 Akorinto 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ifeyo ndife oyenerera. Pakuti mawu a Mulungu sitichita nawo malonda+ ngati mmene ambiri akuchitira,+ koma timalankhula moona mtima monga otsatira Khristu, okhala pamaso pa Mulungu, komanso ngati anthu amene atumidwa ndi Mulungu.+ 2 Petulo 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Komabe, pakati pa anthuwo panadzakhala aneneri onyenga. Momwemonso padzakhala aphunzitsi onyenga pakati panu.+ Amenewa adzabweretsa mwakachetechete timagulu tampatuko towononga ndipo adzakana ngakhale iye amene anawagula,+ n’kudzibweretsera chiwonongeko chofulumira.
18 Pakuti anthu oterowo si akapolo a Ambuye wathu Khristu, koma a mimba zawo.+ Ndipo mwa kulankhula mawu okopa+ ndi achinyengo+ amanyenga anthu oona mtima.
17 Ifeyo ndife oyenerera. Pakuti mawu a Mulungu sitichita nawo malonda+ ngati mmene ambiri akuchitira,+ koma timalankhula moona mtima monga otsatira Khristu, okhala pamaso pa Mulungu, komanso ngati anthu amene atumidwa ndi Mulungu.+
2 Komabe, pakati pa anthuwo panadzakhala aneneri onyenga. Momwemonso padzakhala aphunzitsi onyenga pakati panu.+ Amenewa adzabweretsa mwakachetechete timagulu tampatuko towononga ndipo adzakana ngakhale iye amene anawagula,+ n’kudzibweretsera chiwonongeko chofulumira.