2 Akorinto 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kodi nthawi yonseyi mwakhala mukuganiza kuti tikudzitchinjiriza pamaso panu? Tikulankhula pamaso pa Mulungu mogwirizana ndi Khristu. Komatu okondedwa, tikuchita zonse kuti tikulimbikitseni.+
19 Kodi nthawi yonseyi mwakhala mukuganiza kuti tikudzitchinjiriza pamaso panu? Tikulankhula pamaso pa Mulungu mogwirizana ndi Khristu. Komatu okondedwa, tikuchita zonse kuti tikulimbikitseni.+