2 Akorinto 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma tasiya zinthu zochititsa manyazi zochitikira mseri,+ ndipo sitikuyenda mwachinyengo komanso sitikupotoza mawu a Mulungu.+ Koma pamaso pa Mulungu, takhala chitsanzo chabwino kwa chikumbumtima cha munthu aliyense.+
2 Koma tasiya zinthu zochititsa manyazi zochitikira mseri,+ ndipo sitikuyenda mwachinyengo komanso sitikupotoza mawu a Mulungu.+ Koma pamaso pa Mulungu, takhala chitsanzo chabwino kwa chikumbumtima cha munthu aliyense.+