2 Akorinto 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma tasiya zinthu zochititsa manyazi zochitikira mseri, ndipo sitikuyenda mwachinyengo kapena kupotoza mawu a Mulungu.+ Koma pochititsa choonadi kuti chidziwike, takhala chitsanzo chabwino kwa munthu* aliyense pamaso pa Mulungu.+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:2 Nsanja ya Olonda,8/15/2005, ptsa. 14-1510/1/1997, ptsa. 18-205/1/1997, ptsa. 6-77/15/1990, tsa. 18 Sukulu ya Utumiki, tsa. 153
2 Koma tasiya zinthu zochititsa manyazi zochitikira mseri, ndipo sitikuyenda mwachinyengo kapena kupotoza mawu a Mulungu.+ Koma pochititsa choonadi kuti chidziwike, takhala chitsanzo chabwino kwa munthu* aliyense pamaso pa Mulungu.+
4:2 Nsanja ya Olonda,8/15/2005, ptsa. 14-1510/1/1997, ptsa. 18-205/1/1997, ptsa. 6-77/15/1990, tsa. 18 Sukulu ya Utumiki, tsa. 153