2 Akorinto 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ifeyo ndife oyenerera. Pakuti mawu a Mulungu sitichita nawo malonda+ ngati mmene ambiri akuchitira,+ koma timalankhula moona mtima monga otsatira Khristu, okhala pamaso pa Mulungu, komanso ngati anthu amene atumidwa ndi Mulungu.+ 2 Akorinto 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Sitikuchita chilichonse chokhumudwitsa,+ kuti utumiki wathu usapezedwe chifukwa.+ 2 Akorinto 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho sitikufuna kuti munthu aliyense atipeze chifukwa+ pa zopereka zaufulu+ zimene tikubweretsazi. Agalatiya 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Monga mmene tanenera kale, ndikunenanso kuti, Aliyense amene akulengeza nkhani ina kwa inu monga uthenga wabwino, koma yosiyana ndi imene munalandira,+ ameneyo akhale wotembereredwa.
17 Ifeyo ndife oyenerera. Pakuti mawu a Mulungu sitichita nawo malonda+ ngati mmene ambiri akuchitira,+ koma timalankhula moona mtima monga otsatira Khristu, okhala pamaso pa Mulungu, komanso ngati anthu amene atumidwa ndi Mulungu.+
20 Choncho sitikufuna kuti munthu aliyense atipeze chifukwa+ pa zopereka zaufulu+ zimene tikubweretsazi.
9 Monga mmene tanenera kale, ndikunenanso kuti, Aliyense amene akulengeza nkhani ina kwa inu monga uthenga wabwino, koma yosiyana ndi imene munalandira,+ ameneyo akhale wotembereredwa.