-
Agalatiya 1:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Monga mmene tanenera kale, ndikunenanso kuti, Aliyense amene akulengeza nkhani ina kwa inu nʼkumati ndi uthenga wabwino, koma yosiyana ndi imene munalandira, ameneyo akhale wotembereredwa.
-