Agalatiya 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Monga mmene tanenera kale, ndikunenanso kuti, Aliyense amene akulengeza nkhani ina kwa inu monga uthenga wabwino, koma yosiyana ndi imene munalandira,+ ameneyo akhale wotembereredwa.
9 Monga mmene tanenera kale, ndikunenanso kuti, Aliyense amene akulengeza nkhani ina kwa inu monga uthenga wabwino, koma yosiyana ndi imene munalandira,+ ameneyo akhale wotembereredwa.