Salimo 119:118 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 118 Onse amene amasochera nʼkusiya kutsatira malangizo anu mumawakana,+Chifukwa ndi abodza komanso achinyengo.
118 Onse amene amasochera nʼkusiya kutsatira malangizo anu mumawakana,+Chifukwa ndi abodza komanso achinyengo.