Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 12:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Ukatero umapita kukatenga mizimu ina 7 yoipa kwambiri kuposa umenewo.+ Ikalowa mkatimo imakhala mmenemo ndipo potsirizira pake zochita za munthuyo zimakhala zoipa kwambiri kuposa poyamba.+ Ndi mmenenso zidzakhalira ndi m’badwo woipawu.”+

  • Yohane 5:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kenako Yesu anapeza munthu uja m’kachisi ndi kumuuza kuti: “Onatu wachira tsopano. Usakachimwenso, kuti chinachake choopsa kuposa matenda chisadzakuchitikire.”

  • 2 Petulo 2:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ndithudi, ngati anapulumuka ku zoipitsa za dzikoli+ mwa kumudziwa molondola Ambuye ndi Mpulumutsi Yesu Khristu, koma alowereranso m’zinthu zomwe zija ndi kugonjetsedwa nazo,+ potsirizira pake makhalidwe awo amakhala oipa kwambiri kuposa poyamba.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena