Salimo 56:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndimadalira Mulungu. Sindidzaopa.+Kodi munthu wochokera kufumbi angandichite chiyani?+ Salimo 118:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova ali kumbali yanga, sindidzaopa.+Munthu wochokera kufumbi angandichite chiyani?+ Danieli 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ngati mungatiponyere m’ng’anjo yoyaka moto, Mulungu wathu amene tikumutumikira akhoza kutipulumutsa. Iye atipulumutsa m’ng’anjo yoyaka moto ndiponso m’manja mwanu mfumu.+ Luka 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komanso ndikukuuzani ndithu, mabwenzi anga,+ Musamaope amene amapha thupi lokha, amene sangathe kuchita zoposa pamenepa.+
17 Ngati mungatiponyere m’ng’anjo yoyaka moto, Mulungu wathu amene tikumutumikira akhoza kutipulumutsa. Iye atipulumutsa m’ng’anjo yoyaka moto ndiponso m’manja mwanu mfumu.+
4 Komanso ndikukuuzani ndithu, mabwenzi anga,+ Musamaope amene amapha thupi lokha, amene sangathe kuchita zoposa pamenepa.+