Salimo 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova ndiye kuwala+ kwanga ndi chipulumutso changa.+Ndingaopenso ndani?+Yehova ndiye malo a chitetezo cha moyo wanga.+Ndingachitenso mantha ndi ndani?+ Yesaya 51:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Ndimvereni, inu odziwa chilungamo, inu amene muli ndi lamulo langa mumtima mwanu.+ Musaope chitonzo cha anthu ndipo musachite mantha chifukwa cha mawu awo onyoza.+
27 Yehova ndiye kuwala+ kwanga ndi chipulumutso changa.+Ndingaopenso ndani?+Yehova ndiye malo a chitetezo cha moyo wanga.+Ndingachitenso mantha ndi ndani?+
7 “Ndimvereni, inu odziwa chilungamo, inu amene muli ndi lamulo langa mumtima mwanu.+ Musaope chitonzo cha anthu ndipo musachite mantha chifukwa cha mawu awo onyoza.+