Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 37:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Chilamulo cha Mulungu wake chili mumtima mwake.+

      Poyenda mapazi ake sadzaterereka.+

  • Salimo 119:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  11 Ndasunga mosamala mawu anu mumtima mwanga,+

      Kuti ndisakuchimwireni.+

  • Yeremiya 31:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 “Pangano+ limene ndidzapangane ndi nyumba ya Isiraeli pambuyo pa masiku amenewo ndi ili:+ Ndidzaika chilamulo changa mwa iwo+ ndipo ndidzachilemba mumtima mwawo.+ Ine ndidzakhala Mulungu wawo ndipo iwo adzakhala anthu anga,”+ watero Yehova.

  • 2 Akorinto 3:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pakuti zikuonekeratu kuti ndinu kalata yochokera kwa Khristu yolembedwa ndi ifeyo kudzera mu utumiki wathu.+ Kalatayo siyolembedwa ndi inki koma ndi mzimu+ wa Mulungu wamoyo. Siyolembedwa pazolembapo zamiyala,+ koma zamnofu, pamitima.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena