Miyambo 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Usasiye kukoma mtima kosatha ndi choonadi.+ Uzimange m’khosi mwako+ ndiponso uzilembe pamtima pako.+ Miyambo 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uwamange kuzala zako,+ ndipo uwalembe pamtima pako.+ Ezekieli 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ ndipo ndidzaika mzimu watsopano mwa iwo.+ Ndidzachotsa mtima wamwala m’matupi awo+ n’kuwapatsa mtima wamnofu,+ Ezekieli 36:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndidzakupatsani mtima watsopano,+ ndipo ndidzaika mzimu watsopano mwa inu.+ Ndidzakuchotserani mtima wanu wamwala n’kukupatsani mtima wamnofu.+
3 Usasiye kukoma mtima kosatha ndi choonadi.+ Uzimange m’khosi mwako+ ndiponso uzilembe pamtima pako.+
19 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ ndipo ndidzaika mzimu watsopano mwa iwo.+ Ndidzachotsa mtima wamwala m’matupi awo+ n’kuwapatsa mtima wamnofu,+
26 Ndidzakupatsani mtima watsopano,+ ndipo ndidzaika mzimu watsopano mwa inu.+ Ndidzakuchotserani mtima wanu wamwala n’kukupatsani mtima wamnofu.+