2 Akorinto 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti zikuonekeratu kuti ndinu kalata yochokera kwa Khristu yolembedwa ndi ifeyo kudzera mu utumiki wathu.+ Kalatayo siyolembedwa ndi inki koma ndi mzimu+ wa Mulungu wamoyo. Siyolembedwa pazolembapo zamiyala,+ koma zamnofu, pamitima.+ Aheberi 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Pangano limene ndidzapanga nawo pambuyo pa pangano loyamba lija ndi ili: Ndidzaika malamulo anga m’mitima yawo ndi kuwalemba m’maganizo mwawo,’ watero Yehova,”+
3 Pakuti zikuonekeratu kuti ndinu kalata yochokera kwa Khristu yolembedwa ndi ifeyo kudzera mu utumiki wathu.+ Kalatayo siyolembedwa ndi inki koma ndi mzimu+ wa Mulungu wamoyo. Siyolembedwa pazolembapo zamiyala,+ koma zamnofu, pamitima.+
16 “‘Pangano limene ndidzapanga nawo pambuyo pa pangano loyamba lija ndi ili: Ndidzaika malamulo anga m’mitima yawo ndi kuwalemba m’maganizo mwawo,’ watero Yehova,”+