Salimo 56:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Popeza kuti ndine wogwirizana ndi Mulungu, ndidzatamanda mawu ake.+Ine ndimadalira Mulungu, sindidzaopa.+Kodi munthu angandichite chiyani?+ Aheberi 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Moti tikhale olimba mtima ndithu+ ndipo tinene kuti: “Yehova* ndiye mthandizi wanga. Sindidzaopa. Munthu angandichite chiyani?”+
4 Popeza kuti ndine wogwirizana ndi Mulungu, ndidzatamanda mawu ake.+Ine ndimadalira Mulungu, sindidzaopa.+Kodi munthu angandichite chiyani?+
6 Moti tikhale olimba mtima ndithu+ ndipo tinene kuti: “Yehova* ndiye mthandizi wanga. Sindidzaopa. Munthu angandichite chiyani?”+