2 Mbiri 32:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iyo ikudalira mphamvu za anthu,*+ koma ife tili ndi Yehova Mulungu wathu+ kuti atithandize ndi kutimenyera nkhondo zathu.”+ Pamenepo anthuwo anayamba kulimba mtima chifukwa cha mawu a Hezekiya mfumu ya Yuda.+ Salimo 118:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova ali kumbali yanga, sindidzaopa.+Munthu wochokera kufumbi angandichite chiyani?+
8 Iyo ikudalira mphamvu za anthu,*+ koma ife tili ndi Yehova Mulungu wathu+ kuti atithandize ndi kutimenyera nkhondo zathu.”+ Pamenepo anthuwo anayamba kulimba mtima chifukwa cha mawu a Hezekiya mfumu ya Yuda.+