Salimo 56:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Popeza kuti ndine wogwirizana ndi Mulungu,+ ndidzatamanda mawu ake.Popeza kuti ndine wogwirizana ndi Yehova, ndidzatamanda mawu ake.+ Salimo 119:160 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 160 Mawu anu onse ndi choonadi chokhachokha,+Ndipo chigamulo chanu chilichonse cholungama chidzakhalapo mpaka kalekale.+
10 Popeza kuti ndine wogwirizana ndi Mulungu,+ ndidzatamanda mawu ake.Popeza kuti ndine wogwirizana ndi Yehova, ndidzatamanda mawu ake.+
160 Mawu anu onse ndi choonadi chokhachokha,+Ndipo chigamulo chanu chilichonse cholungama chidzakhalapo mpaka kalekale.+