Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 45:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Yehova wanena kuti: “Antchito osalipidwa a ku Iguputo,+ amalonda a ku Itiyopiya, ndi Asabeya,+ amuna ataliatali,+ adzabwera kwa iwe ndipo adzakhala ako.+ Iwo adzayenda pambuyo pako. Adzabwera kwa iwe atamangidwa m’matangadza+ ndipo adzakugwadira.+ Adzapemphera kwa iwe kuti, ‘Zoonadi Mulungu ali ndi iwe+ ndipo palibenso wina. Palibenso Mulungu wina.’”+

  • Yeremiya 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Inu Yehova, mumandidziwa bwino.+ Mumandiona ndipo mumasanthula mtima wanga kuti muone ngati uli wokhulupirika kwa inu.+ Apatuleni ngati nkhosa zimene zikukaphedwa,+ ndipo aikeni padera kuyembekezera tsiku lokaphedwa.

  • Yohane 10:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Koma ngati ndikuzichita, ngakhale simukundikhulupirira, khulupirirani ntchitozo,+ kuti mudziwe ndi kupitirizabe kudziwa kuti Atate ndi ine ndife ogwirizana.”+

  • Yohane 17:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 kuti onsewa akhale amodzi,+ mmene inu Atate ndi ine tilili ogwirizana,+ kuti iwonso akhale ogwirizana ndi ife,+ ndi kuti dziko likhulupirire kuti inu munanditumadi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena