Aroma 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 momwemonso ifeyo, ngakhale kuti ndife ambiri, tili thupi limodzi+ mwa Khristu, ndipo aliyense payekha ndi chiwalo cha mnzake.+ 1 Akorinto 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano ndikukudandaulirani+ abale, m’dzina+ la Ambuye wathu Yesu Khristu, kuti nonse muzilankhula mogwirizana ndi kuti pasakhale magawano+ pakati panu, koma kuti mukhale ogwirizana+ pokhala ndi mtima umodzi ndi maganizo amodzi.+ Agalatiya 3:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Palibe Myuda kapena Mgiriki,+ palibe kapolo kapena mfulu,+ palibenso mwamuna kapena mkazi.+ Nonsenu ndinu munthu mmodzi mwa Khristu Yesu.+ 1 Yohane 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Komatu, ngati tikuyenda m’kuunika ngati mmene iye alili m’kuunika,+ ndiye kuti ndife ogwirizana,+ ndipo magazi+ a Yesu Mwana wake akutiyeretsa+ ku uchimo wonse.+
5 momwemonso ifeyo, ngakhale kuti ndife ambiri, tili thupi limodzi+ mwa Khristu, ndipo aliyense payekha ndi chiwalo cha mnzake.+
10 Tsopano ndikukudandaulirani+ abale, m’dzina+ la Ambuye wathu Yesu Khristu, kuti nonse muzilankhula mogwirizana ndi kuti pasakhale magawano+ pakati panu, koma kuti mukhale ogwirizana+ pokhala ndi mtima umodzi ndi maganizo amodzi.+
28 Palibe Myuda kapena Mgiriki,+ palibe kapolo kapena mfulu,+ palibenso mwamuna kapena mkazi.+ Nonsenu ndinu munthu mmodzi mwa Khristu Yesu.+
7 Komatu, ngati tikuyenda m’kuunika ngati mmene iye alili m’kuunika,+ ndiye kuti ndife ogwirizana,+ ndipo magazi+ a Yesu Mwana wake akutiyeretsa+ ku uchimo wonse.+