1 Akorinto 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti ndi mzimu umodzi, tonsefe tinabatizidwa+ kukhala thupi limodzi, kaya tikhale Ayuda kapena Agiriki, akapolo kapena mfulu, ndipo tonsefe tinamwetsedwa+ mzimu umodzi. Akolose 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mukatero, sipadzakhala Mgiriki kapena Myuda, kudulidwa kapena kusadulidwa, mlendo, Msukuti, kapolo, kapena mfulu,+ koma Khristu ndiye zinthu zonse ndipo ali mwa onse.+
13 Pakuti ndi mzimu umodzi, tonsefe tinabatizidwa+ kukhala thupi limodzi, kaya tikhale Ayuda kapena Agiriki, akapolo kapena mfulu, ndipo tonsefe tinamwetsedwa+ mzimu umodzi.
11 Mukatero, sipadzakhala Mgiriki kapena Myuda, kudulidwa kapena kusadulidwa, mlendo, Msukuti, kapolo, kapena mfulu,+ koma Khristu ndiye zinthu zonse ndipo ali mwa onse.+